Ekisodo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Isiraeli anaberekana ndipo anachuluka m’dzikomo. Iwo anapitiriza kuchulukana ndi kukhala amphamvu koposa, moti anadzaza m’dzikomo.+ Deuteronomo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+ Salimo 105:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu anachititsa anthu ake kuberekana,+Ndipo pang’onopang’ono anawasandutsa anthu amphamvu kuposa adani awo.+ Machitidwe 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Nthawi itayandikira, yakuti lonjezo likwaniritsidwe limene Mulungu anapereka kwa Abulahamu, mtundu wa anthu unakula ndi kuwonjezeka mu Iguputo.+
7 Ana a Isiraeli anaberekana ndipo anachuluka m’dzikomo. Iwo anapitiriza kuchulukana ndi kukhala amphamvu koposa, moti anadzaza m’dzikomo.+
22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+
24 Mulungu anachititsa anthu ake kuberekana,+Ndipo pang’onopang’ono anawasandutsa anthu amphamvu kuposa adani awo.+
17 “Nthawi itayandikira, yakuti lonjezo likwaniritsidwe limene Mulungu anapereka kwa Abulahamu, mtundu wa anthu unakula ndi kuwonjezeka mu Iguputo.+