-
Genesis 27:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Tsopano Yakobo anapita kumene kunali bambo ake n’kunena kuti: “Bambo!” Ndipo Isaki anayankha kuti: “Ine pano! Ndiwe ndani kodi mwana wanga?”
-