Genesis 41:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chaka cha njala chisanafike, Yosefe anakhala ndi ana aamuna awiri,+ amene anam’berekera mkazi wake Asenati, mwana wa Potifera, wansembe wa mzinda wa Oni.
50 Chaka cha njala chisanafike, Yosefe anakhala ndi ana aamuna awiri,+ amene anam’berekera mkazi wake Asenati, mwana wa Potifera, wansembe wa mzinda wa Oni.