Genesis 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino. Genesis 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo analowa pamodzi ndi nyama zakutchire zamtundu uliwonse,+ nyama zoweta zamtundu uliwonse, nyama zokwawa* pansi zamtundu uliwonse,+ zolengedwa zouluka zamtundu uliwonse,+ ndiponso mbalame zilizonse ndi zolengedwa zilizonse zamapiko.+
25 Motero Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zoweta monga mwa mitundu yake, komanso nyama iliyonse yokwawa panthaka monga mwa mtundu wake.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.
14 Iwo analowa pamodzi ndi nyama zakutchire zamtundu uliwonse,+ nyama zoweta zamtundu uliwonse, nyama zokwawa* pansi zamtundu uliwonse,+ zolengedwa zouluka zamtundu uliwonse,+ ndiponso mbalame zilizonse ndi zolengedwa zilizonse zamapiko.+