Maliko 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kuyambira pa chiyambi pa chilengedwe, ‘Mulungu anawalenga mwamuna ndi mkazi.+ 1 Akorinto 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso mwamuna sanalengedwere mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.+