Rute 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Boazi anapita kuchipata.+ Kumeneko iye anakhala pansi. Ali chikhalire choncho, anaona wowombola anam’tchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe Uje takhotera pano, khala pansi apa.” Motero anakhota n’kukhala pansi. Esitere 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamene anamwali+ anasonkhanitsidwa pamodzi kachiwiri, Moredekai anali atakhala pansi kuchipata cha mfumu.+
4 Zitatero, Boazi anapita kuchipata.+ Kumeneko iye anakhala pansi. Ali chikhalire choncho, anaona wowombola anam’tchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe Uje takhotera pano, khala pansi apa.” Motero anakhota n’kukhala pansi.
19 Pamene anamwali+ anasonkhanitsidwa pamodzi kachiwiri, Moredekai anali atakhala pansi kuchipata cha mfumu.+