Genesis 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atakweza maso,+ anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye. Atawaona, ananyamuka pakhomo la hemayo n’kuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada n’kuwaweramira mpaka nkhope yake pansi.+ 1 Samueli 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
2 Atakweza maso,+ anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye. Atawaona, ananyamuka pakhomo la hemayo n’kuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada n’kuwaweramira mpaka nkhope yake pansi.+
8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+