Yoswa 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero, anyamata amene anakazonda dziko aja, anapita kukatulutsa Rahabi, bambo ake, mayi ake, alongo ake, ndi onse amene anali naye. Anatulutsa achibale ake onse,+ ndipo anawapatsa malo kunja kwa msasa wa Isiraeli. 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
23 Chotero, anyamata amene anakazonda dziko aja, anapita kukatulutsa Rahabi, bambo ake, mayi ake, alongo ake, ndi onse amene anali naye. Anatulutsa achibale ake onse,+ ndipo anawapatsa malo kunja kwa msasa wa Isiraeli.
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+