Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano, chonde lumbirani kwa ine pali Yehova,+ kuti chifukwa choti ndakusonyezani kukoma mtima kosatha, inunso mudzasonyeza anthu a m’nyumba ya bambo anga+ kukoma mtima kosatha, ndipo mundipatse chizindikiro chodalirika.+

  • 1 Samueli 20:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Pamenepo Yonatani anauza Davide kuti: “Pita mu mtendere,+ pakuti tonse awiri talumbira+ m’dzina la Yehova kuti, ‘Yehova akhale pakati pa iwe ndi ine, ndi pakati pa ana ako ndi ana anga mpaka kalekale.’”+

      Chotero Davide ananyamuka ndi kupita, koma Yonatani anabwerera kumzinda.

  • Yeremiya 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena