Deuteronomo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mu limodzi la mafuko anu, ndipo muzichita zonse zimene ndakulamulani pamalo amenewo.+
14 Koma muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mu limodzi la mafuko anu, ndipo muzichita zonse zimene ndakulamulani pamalo amenewo.+