Yobu 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anaika malire ozungulira pamwamba pa madzi,+Kumene kuwala kumakathera mu mdima. 2 Akorinto 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Mulungu ndiye anati: “Kuwala kuunike kuchokera mu mdima,”+ ndipo kudzera mwa nkhope ya Khristu,+ waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudzana ndi kudziwa+ Mulungu.
6 Pakuti Mulungu ndiye anati: “Kuwala kuunike kuchokera mu mdima,”+ ndipo kudzera mwa nkhope ya Khristu,+ waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudzana ndi kudziwa+ Mulungu.