Levitiko 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mukalowa m’dziko limene ndikukupatsani, n’kukolola mbewu za m’dzikomo, muzibweretsa kwa wansembe mtolo umodzi wa zipatso zanu zoyambirira.+ Numeri 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Ndipo pa tsiku la zipatso zoyambirira,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova, paphwando lanu la masabata,+ muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+ Deuteronomo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Uziwerenga masabata 7. Uziyamba kuwerenga masabata 7 amenewo kuchokera pamene wayamba kumweta tirigu.+ Machitidwe 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano pa tsiku la chikondwerero cha Pentekosite,+ onse anali atasonkhana pamalo amodzi.
10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mukalowa m’dziko limene ndikukupatsani, n’kukolola mbewu za m’dzikomo, muzibweretsa kwa wansembe mtolo umodzi wa zipatso zanu zoyambirira.+
26 “‘Ndipo pa tsiku la zipatso zoyambirira,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova, paphwando lanu la masabata,+ muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+
9 “Uziwerenga masabata 7. Uziyamba kuwerenga masabata 7 amenewo kuchokera pamene wayamba kumweta tirigu.+