Ekisodo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+ Levitiko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyama ya nsembe zachiyanjano zoperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge iliyonse ya nyamayo kufika m’mawa.+
10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+
15 Nyama ya nsembe zachiyanjano zoperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge iliyonse ya nyamayo kufika m’mawa.+