Numeri 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Potsirizira pake, tinalirira Yehova.+ Iye anamva kulira kwathu, ndipo anatitumizira mngelo+ n’kutitulutsa m’dziko la Iguputo. Tsopano tili kuno ku Kadesi, mzinda umene uli m’malire a dziko lanu.
16 Potsirizira pake, tinalirira Yehova.+ Iye anamva kulira kwathu, ndipo anatitumizira mngelo+ n’kutitulutsa m’dziko la Iguputo. Tsopano tili kuno ku Kadesi, mzinda umene uli m’malire a dziko lanu.