4 “Yehova Mulungu wanu akadzawakankhira kutali ndi inu musadzanene mumtima mwanu kuti, ‘Yehova watilowetsa m’dziko lino kuti tilitenge kukhala lathu, chifukwa cha kulungama kwathu,’+ pamene kwenikweni Yehova akukankhira mitundu iyi kutali ndi inu chifukwa cha kuipa kwawo.+