Deuteronomo 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iweyo pita pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena. Iweyo ndiye udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzakuuza,+ ndipo tidzamvera ndi kuchita zomwezo.’ Yoswa 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo Yoswa anauza anthuwo kuti: “Inu ndinu mboni mwa kufuna kwanu,+ zotsimikizira kuti mwasankha nokha kutumikira Yehova.”+ Ndiyeno anthuwo anati: “Inde! Ndife mboni.”
27 Iweyo pita pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena. Iweyo ndiye udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu adzakuuza,+ ndipo tidzamvera ndi kuchita zomwezo.’
22 Pamenepo Yoswa anauza anthuwo kuti: “Inu ndinu mboni mwa kufuna kwanu,+ zotsimikizira kuti mwasankha nokha kutumikira Yehova.”+ Ndiyeno anthuwo anati: “Inde! Ndife mboni.”