Aheberi 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye chifukwa chake ngakhale pangano loyamba+ lija silinakhazikitsidwe popanda magazi.+