Deuteronomo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 pamene Aisiraeli onse afika kudzaona nkhope ya Yehova+ Mulungu wanu pamalo amene iye adzasankhe,+ muziwerenga chilamulo ichi pamaso pa Aisiraeli onse m’makutu mwawo.+ Machitidwe 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.”
11 pamene Aisiraeli onse afika kudzaona nkhope ya Yehova+ Mulungu wanu pamalo amene iye adzasankhe,+ muziwerenga chilamulo ichi pamaso pa Aisiraeli onse m’makutu mwawo.+
15 Chilamulo ndi Zolemba za aneneri zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri+ a sunagoge anawatumizira mawu akuti: “Amuna inu, abale athu, ngati muli ndi mawu alionse olimbikitsa nawo anthu, lankhulani.”