Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Aroni atangomaliza kulankhula ndi khamu lonse la ana a Isiraeli, iwo anatembenuka ndi kuyang’ana kuchipululu. Ndipo taonani! Ulemerero wa Yehova unaonekera mumtambo.+

  • Levitiko 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo Mose ndi Aroni analowa m’chihema chokumanako, kenako anatulukamo n’kudalitsa anthuwo.+

      Atatero, ulemerero wa Yehova+ unaonekera kwa anthu onse,

  • Numeri 16:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Khamulo litasonkhana pamodzi kuti liukire Mose ndi Aroni, linacheukira kuchihema chokumanako. Anthuwo anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho, ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+

  • Ezekieli 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Panali chinachake chooneka ngati utawaleza+ umene umaoneka mumtambo pa tsiku la mvula yamphamvu. Umu ndi mmene kuwala kozungulira pamalopo kunali kuonekera. Zinali kuoneka ngati ulemerero wa Yehova.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+ Kenako ndinayamba kumva mawu a winawake akulankhula.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena