Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+
5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+