Ekisodo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Yehova anatsikira paphiri la Sinai, pamwamba pa phirilo. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo, ndipo Mose anakweradi.+
20 Pamenepo Yehova anatsikira paphiri la Sinai, pamwamba pa phirilo. Kenako Yehova anaitana Mose kuti akwere pamwamba pa phirilo, ndipo Mose anakweradi.+