Numeri 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Azinyamula nsalu za chihema chopatulika+ ndi chihema chokumanako,+ ndiponso chophimba chake,+ chophimba cha chikopa cha katumbu+ chomwe chili pamwamba pake, ndi nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chokumanako. 1 Mbiri 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide atangoyamba kukhala m’nyumba yake,+ anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ koma likasa+ la pangano la Yehova likukhala m’chihema chansalu.”+
25 Azinyamula nsalu za chihema chopatulika+ ndi chihema chokumanako,+ ndiponso chophimba chake,+ chophimba cha chikopa cha katumbu+ chomwe chili pamwamba pake, ndi nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chokumanako.
17 Ndiyeno Davide atangoyamba kukhala m’nyumba yake,+ anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ koma likasa+ la pangano la Yehova likukhala m’chihema chansalu.”+