Ekisodo 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nsalu zisanu anazilumikiza,+ ndipo anachita chimodzimodzi ndi nsalu zinanso zisanu.