Ekisodo 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndi zitsulo zake 40 zasiliva zokhazikapo mafelemuwo. Zitsulo ziwiri zinali zokhazikapo felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri zokhazikapo felemu lina la mano awiri.+
26 ndi zitsulo zake 40 zasiliva zokhazikapo mafelemuwo. Zitsulo ziwiri zinali zokhazikapo felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri zokhazikapo felemu lina la mano awiri.+