Ekisodo 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako anapanga mafelemu oimika a chihema chopatulika a matabwa a mthethe.+ Ekisodo 36:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo kumbuyo kwa chihema chopatulika, chakumadzulo, anapangirako mafelemu 6.+