Ekisodo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyankha iye anati: “Anakuika iwe ndani kukhala kalonga ndi woweruza wathu?+ Kodi ukufuna kundipha mmene unaphera Mwiguputo uja?”+ Pamenepo Mose anachita mantha ndipo anati mumtima mwake: “Haa! Nkhani ija yadziwika.”+ Machitidwe 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mose anali kuganiza kuti abale akewo azindikira kuti Mulungu akuwapatsa chipulumutso kudzera m’dzanja lake,+ koma iwo sanaizindikire mfundo imeneyi.
14 Poyankha iye anati: “Anakuika iwe ndani kukhala kalonga ndi woweruza wathu?+ Kodi ukufuna kundipha mmene unaphera Mwiguputo uja?”+ Pamenepo Mose anachita mantha ndipo anati mumtima mwake: “Haa! Nkhani ija yadziwika.”+
25 Mose anali kuganiza kuti abale akewo azindikira kuti Mulungu akuwapatsa chipulumutso kudzera m’dzanja lake,+ koma iwo sanaizindikire mfundo imeneyi.