Ekisodo 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo kumbali inanso ya chipata cha bwalolo, mpandawo unali mikono 15 kutalika kwake. Zinali choncho kumbali iyi ya chipata komanso kumbali inayo. Kunali nsanamira zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo nsanamirazo.+
15 Ndipo kumbali inanso ya chipata cha bwalolo, mpandawo unali mikono 15 kutalika kwake. Zinali choncho kumbali iyi ya chipata komanso kumbali inayo. Kunali nsanamira zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo nsanamirazo.+