-
Ekisodo 38:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mizati yake inayi ndi zitsulo zinayi zokhazikapo mizatiyo zinali zamkuwa. Tizitsulo ta mizatiyo tokolowekapo nsalu tinali tasiliva, ndipo mitu ya mizatiyo ndi tizitsulo tolumikizira anazikuta ndi siliva.
-