Ekisodo 39:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anabweretsanso choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino, nyale zake zondandalikidwa bwino,+ ziwiya zonse za choikapo nyalecho,+ mafuta a nyale,+ Levitiko 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira+ oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale iziyaka nthawi zonse.+
37 Anabweretsanso choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino, nyale zake zondandalikidwa bwino,+ ziwiya zonse za choikapo nyalecho,+ mafuta a nyale,+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira+ oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale iziyaka nthawi zonse.+