Genesis 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Golide wa dziko limenelo ndi wabwino.+ Kulinso mafuta onunkhira a bedola+ ndi miyala yamtengo wapatali ya onekisi.+ Ekisodo 35:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 miyala ya onekisi, miyala yozika pa efodi*+ ndi pachovala pachifuwa.+
12 Golide wa dziko limenelo ndi wabwino.+ Kulinso mafuta onunkhira a bedola+ ndi miyala yamtengo wapatali ya onekisi.+