-
Levitiko 8:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 M’dengu la mikate yosafufumitsa limene linali pamaso pa Yehova, anatengamo mtanda umodzi wa mkate wozungulira woboola pakati,+ mtanda umodzi wa mkate wozungulira woboola pakati wothira mafuta,+ ndi kamtanda kamodzi ka mkate kopyapyala.+ Anaziika pamwamba pa mafuta ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja.
-