Ekisodo 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga+ khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ya ulusi wofiira kwambiri, ndi ya ulusi wopota wabwino kwambiri. Ekisodo 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atatero anakoloweka nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chopatulika. Levitiko 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno usonkhanitse khamu lonse+ pakhomo la chihema chokumanako.”+
36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga+ khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ya ulusi wofiira kwambiri, ndi ya ulusi wopota wabwino kwambiri.