Ekisodo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndipo uveke Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwapatse mphamvu*+ ndi kuwayeretsa, ndipo atumikire monga ansembe anga. Ekisodo 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero Mose anati: “Dzilimbitseni* lero kuti muchite utumiki kwa Yehova,+ chifukwa aliyense wa inu waukira mwana wake ndi m’bale wake,+ kuti Mulungu akupatseni dalitso lero.”+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+
41 Ndipo uveke Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwapatse mphamvu*+ ndi kuwayeretsa, ndipo atumikire monga ansembe anga.
29 Zitatero Mose anati: “Dzilimbitseni* lero kuti muchite utumiki kwa Yehova,+ chifukwa aliyense wa inu waukira mwana wake ndi m’bale wake,+ kuti Mulungu akupatseni dalitso lero.”+