Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno azitsuka matumbo+ ndi ziboda+ ndi madzi. Kenako wansembe azitenga nyama yonseyo ndi kuitentha+ paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yopsereza, nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+

  • Levitiko 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anatenganso matumbo ndi ziboda n’kuzitsuka ndi madzi. Ndiyeno Mose anatentha nkhosa yonseyo paguwa lansembe.+ Inali nsembe yopsereza yafungo lokhazika mtima pansi.+ Komanso, inali nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova, monga mmene Yehova analamulira Mose.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena