Levitiko 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu wamba* asadye chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala m’nyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chopatulika chilichonse. Numeri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+ Mateyu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+
10 “‘Munthu wamba* asadye chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala m’nyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chopatulika chilichonse.
10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+
4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+