Levitiko 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mose anachita monga mmene Yehova anam’lamulira. Ndipo khamu lonse linasonkhana pakhomo+ la chihema chokumanako.
4 Mose anachita monga mmene Yehova anam’lamulira. Ndipo khamu lonse linasonkhana pakhomo+ la chihema chokumanako.