Ekisodo 30:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndipo uziyeretse kuti zikhale zoyera koposa.+ Aliyense wogwira zinthu zimenezi azikhala woyera.+ Mateyu 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akhungu inu! Chofunika kwambiri n’chiti, mphatso kapena guwa lansembe+ limene limayeretsa mphatsoyo?
19 Akhungu inu! Chofunika kwambiri n’chiti, mphatso kapena guwa lansembe+ limene limayeretsa mphatsoyo?