Ekisodo 16:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Tsopano miyezo 10 ya omeri inali kukwana muyezo umodzi wa efa.* Numeri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+
5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+