50 Tsopano lolani kuti aliyense wa ife apereke zimene wabwera nazo monga chopereka kwa Yehova,+ zinthu zagolide, matcheni ovala m’miyendo, zibangili, mphete zachifumu,+ ndolo, ndi zodzikongoletsera zina za akazi.+ Tipereke zimenezi kwa Yehova kuti ziphimbe machimo athu.”