Salimo 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+
8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+