Ekisodo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime.
15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime.