Yoswa 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ansembewo akadzaliza malipenga a nyanga za nkhosa, ndipo inu mukadzamva kulira kwa malipengawo, nonse mudzafuule mfuu yankhondo mwamphamvu,+ ndipo mpanda wonse wa mzindawo udzagwa pansi.+ Pamenepo, nonsenu mudzathamangire kumeneko.” Amosi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzayatsa mpanda wa Raba+ ndipo motowo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo. Padzakhala chizindikiro chochenjeza pa tsiku la nkhondo ndiponso mphepo yamkuntho pa tsiku la chimvula champhamvu.+
5 Ansembewo akadzaliza malipenga a nyanga za nkhosa, ndipo inu mukadzamva kulira kwa malipengawo, nonse mudzafuule mfuu yankhondo mwamphamvu,+ ndipo mpanda wonse wa mzindawo udzagwa pansi.+ Pamenepo, nonsenu mudzathamangire kumeneko.”
14 Ndidzayatsa mpanda wa Raba+ ndipo motowo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo. Padzakhala chizindikiro chochenjeza pa tsiku la nkhondo ndiponso mphepo yamkuntho pa tsiku la chimvula champhamvu.+