Deuteronomo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ndinatenga miyala iwiriyo ndi kuiponya pansi mwamphamvu ndi manja anga, ndi kuiswa inu mukuona.+
17 Pamenepo ndinatenga miyala iwiriyo ndi kuiponya pansi mwamphamvu ndi manja anga, ndi kuiswa inu mukuona.+