Deuteronomo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+ Malaki 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndakutumizirani lamulo limeneli+ kuti pangano+ limene ndinapangana ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa makamu.
9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+
4 Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndakutumizirani lamulo limeneli+ kuti pangano+ limene ndinapangana ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa makamu.