Machitidwe 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho iwo anapanga mwana wa ng’ombe m’masiku amenewo,+ ndi kubweretsa nsembe kwa fano limenelo. Pamenepo anasangalala ndi ntchito za manja awo.+
41 Choncho iwo anapanga mwana wa ng’ombe m’masiku amenewo,+ ndi kubweretsa nsembe kwa fano limenelo. Pamenepo anasangalala ndi ntchito za manja awo.+