Luka 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwadzidzidzi mngelo wa Yehova+ anaima chapafupi ndi iwo, ndipo ulemerero wa Yehova+ unawawalira ponsepo, mwakuti anachita mantha kwambiri. Machitidwe 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu. Machitidwe 7:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 inu amene munalandira Chilamulo kudzera mwa angelo,+ koma osachisunga.”
9 Mwadzidzidzi mngelo wa Yehova+ anaima chapafupi ndi iwo, ndipo ulemerero wa Yehova+ unawawalira ponsepo, mwakuti anachita mantha kwambiri.
38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.