Deuteronomo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo Yehova anandipatsa miyala iwiri yosema imene chala cha Mulungu chinalembapo.+ Pamiyala iwiri imeneyi panali mawu onse amene Yehova analankhula nanu m’phiri, kuchokera pakati pa moto, tsiku limene munasonkhana kumeneko.+ 2 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+
10 ndipo Yehova anandipatsa miyala iwiri yosema imene chala cha Mulungu chinalembapo.+ Pamiyala iwiri imeneyi panali mawu onse amene Yehova analankhula nanu m’phiri, kuchokera pakati pa moto, tsiku limene munasonkhana kumeneko.+
3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+