Ekisodo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova anauzanso Mose kuti: “Ndawayang’ana anthu amenewa, ndipo ndaona kuti ndi anthu ouma khosi.+ Ekisodo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mupite kudziko loyenda mkaka ndi uchi,+ pakuti sindidzayenda pakati panu, pakuti ndingakufafanizeni panjira,+ chifukwa ndinu anthu ouma khosi.”+
3 Mupite kudziko loyenda mkaka ndi uchi,+ pakuti sindidzayenda pakati panu, pakuti ndingakufafanizeni panjira,+ chifukwa ndinu anthu ouma khosi.”+