Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Samala. Uzimvera mawu onsewa amene ndikukuuza,+ kuti zinthu zikuyendere bwino+ mpaka kalekale, iweyo ndi ana ako aamuna obwera m’mbuyo mwako, chifukwa ukatero udzachita chabwino ndi choyenera pamaso pa Yehova Mulungu wako.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
28 “Samala. Uzimvera mawu onsewa amene ndikukuuza,+ kuti zinthu zikuyendere bwino+ mpaka kalekale, iweyo ndi ana ako aamuna obwera m’mbuyo mwako, chifukwa ukatero udzachita chabwino ndi choyenera pamaso pa Yehova Mulungu wako.+