Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakhale ndi milungu ina iliyonse+ kupatulapo ine.* 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+ 1 Yohane 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu ana okondedwa, pewani mafano.+